1 A Song of Ascents. Look! Praise the LORD, all you servants of the LORD, who stand by night in the LORD’s house!
Nyimbo yoyimba pokwera ku Yerusalemu. Bwerani, mutamande Yehova, inu atumiki onse a Yehova, amene mumatumikira usiku mʼnyumba ya Yehova.