< Masalimo 117 >

1 Tamandani Yehova, inu anthu a mitundu yonse; mulemekezeni Iye, inu mitundu ya anthu.
הללו את-יהוה כל-גוים שבחוהו כל-האמים
2 Pakuti chikondi chake pa ife ndi chachikulu, ndipo kukhulupirika kwa Yehova nʼkosatha. Tamandani Yehova.
כי גבר עלינו חסדו-- ואמת-יהוה לעולם הללו-יה

< Masalimo 117 >