< 1 Mbiri 8 >

1 Benjamini anabereka Bela mwana wake woyamba, wachiwiri Asibeli, wachitatu Ahara,
Beniamin pak zplodil Bélu, prvorozeného svého, Asbele druhého, Achracha třetího,
2 wachinayi Noha ndipo wachisanu Rafa.
Nocha čtvrtého, Rafa pátého.
3 Ana a Bela anali awa: Adari, Gera, Abihudi,
Béla pak měl syny: Addara, Geru, Abiuda,
4 Abisuwa, Naamani, Ahowa,
Abisua, Námana, Achoacha,
5 Gera, Sefufani ndi Hiramu.
A Geru, Sefufana a Churama.
6 Zidzukulu za Ehudi, zimene zinali atsogoleri a mabanja a amene amakhala ku Geba ndipo zinasamutsidwa kupita ku Manahati zinali izi:
Ti jsou synové Echudovi, ti jsou knížata čeledí otcovských, bydlících v Gabaa, kteříž je uvedli do Manáhat,
7 Naamani, Ahiya ndi Gera, amene anawasamutsa ndipo anabereka Uza ndi Ahihudi.
Totiž: Náman, a Achia a Gera. On přestěhoval je; zplodil pak Uza a Achichuda.
8 Saharaimu anabereka ana ku Mowabu atalekana ndi akazi ake, Husimu ndi Baara.
Sacharaim pak zplodil v krajině Moábské, když onen byl propustil je, s Chusimou a Bárou manželkami svými.
9 Mwa mkazi wake Hodesi anabereka Yobabu, Zibiya, Mesa, Malikamu,
Zplodil s Chodes manželkou svou Jobaba, Sebia, Mésa a Malkama,
10 Yeusi, Sakiya ndi Mirima. Awa ndiye ana ake, atsogoleri a mabanja awo.
Jehuza, Sachia a Mirma. Ti jsou synové jeho, knížata čeledí otcovských.
11 Mwa mkazi wake Husimu anabereka Abitubi ndi Elipaala.
S Chusimou pak byl zplodil Abitoba a Elpále.
12 Ana a Elipaala anali awa: Eberi, Misamu, Semedi (amene anamanga mizinda ya Ono ndi Lodi ndi midzi yake yozungulira)
Synové pak Elpálovi: Heber, Misam a Semer. Ten vystavěl Ono a Lod, i vsi jeho.
13 ndiponso Beriya ndi Sema, amene anali atsogoleri a mabanja a amene ankakhala ku Ayaloni ndipo anathamangitsa nzika za ku Gati.
A Beria a Sema. Ti jsou knížata čeledí otcovských, bydlících v Aialon; ti zahnali obyvatele Gát.
14 Ahiyo, Sasaki, Yeremoti,
Achio pak, Sasák a Jeremot,
15 Zebadiya, Aradi, Ederi,
Zebadiáš, Arad a Ader,
16 Mikayeli, Isipa ndi Yoha anali ana a Beriya.
Michael, Ispa a Jocha synové Beria.
17 Zebadiya, Mesulamu, Hiziki, Heberi,
A Zebadiáš, Mesullam, Chiski, Heber,
18 Isimerai, Iziliya ndi Yobabu anali ana a Elipaala.
Ismerai, Izliáš a Jobab synové Elpálovi.
19 Yakimu, Zikiri, Zabidi,
A Jakim, Zichri a Zabdi.
20 Elienai, Ziletai, Elieli,
Elienai, Ziletai a Eliel,
21 Adaya, Beraya ndi Simirati anali ana a Simei.
Adaiáš, Baraiáš a Simrat synové Simei.
22 Isipani, Eberi, Elieli,
Ispan a Heber a Eliel,
23 Abidoni, Zikiri, Hanani,
Abdon, Zichri a Chanan,
24 Hananiya, Elamu, Anitotiya,
Chananiáš, Elam a Anatotiáš,
25 Ifideya ndi Penueli anali ana a Sasaki.
Ifdaiáš a Fanuel synové Sasákovi.
26 Samuserai, Sehariya, Ataliya,
Samserai, Sechariáš a Ataliáš,
27 Yaaresiya, Eliya ndi Zikiri anali ana a Yerohamu.
Jaresiáš, Eliáš a Zichri synové Jerochamovi.
28 Onsewa anali atsogoleri a mabanja, anthu otchuka potsata mibado yawo, ndipo ankakhala mu Yerusalemu.
Ta jsou knížata otcovských čeledí po rodinách svých, kterážto knížata bydlila v Jeruzalémě.
29 Yeiyeli amene amabereka Gibiyoni ankakhala ku Gibiyoni. Dzina la mkazi wake linali Maaka,
V Gabaon pak bydlilo kníže Gabaon, a jméno manželky jeho Maacha.
30 ndipo mwana wake woyamba anali Abidoni, motsatana ndi Zuri, Kisi, Baala, Neri, Nadabu,
A syn jeho prvorozený Abdon, Zur, Cis, Bál a Nádab,
31 Gedori, Ahiyo, Zekeri
Ale Gedor, Achio, Zecher.
32 ndi Mikiloti, amene anabereka Simea. Iwowa ankakhalanso ku Yerusalemu ndi abale awo.
A Miklot zplodil Simea. I ti také naproti bratřím svým bydlili v Jeruzalémě s bratřími svými.
33 Neri anabereka Kisi. Kisi anabereka Sauli, ndipo Sauli anabereka Yonatani, Maliki-Suwa, Abinadabu ndi Esibaala.
Ner pak zplodil Cisa, a Cis zplodil Saule. Saul pak zplodil Jonatu, Melchisua, Abinadaba a Ezbále.
34 Mwana wa Yonatani anali Meri-Baala, amene anabereka Mika.
Syn pak Jonatův Meribbál, Meribbál pak zplodil Mícha.
35 Ana a Mika anali awa: Pitoni, Meleki, Tareya ndi Ahazi.
Synové pak Míchovi: Piton, Melech, Tarea a Achaz.
36 Ahazi anabereka Yehoyada, Yehoyada anabereka Alemeti, Azimaveti ndi Zimuri, ndipo Zimuri anabereka Moza.
Achaz pak zplodil Jehoadu, Jehoada pak zplodil Alemeta, Azmaveta a Zimru. Zimri pak zplodil Mozu.
37 Moza anabereka Bineya. Ana ake anali Rafa, Eleasa ndi Azeli.
Moza pak zplodil Bina. Ráfa syn jeho, Elasa syn jeho, Azel syn jeho.
38 Azeli anali ndi ana asanu ndi mmodzi, ndipo mayina awo anali awa: Azirikamu, Bokeru, Ismaeli, Seariya, Obadiya ndi Hanani. Onsewa anali ana a Azeli.
Azel pak měl šest synů, jichž tato jsou jména: Azrikam, Bochru, Izmael, Seariáš a Abdiáš a Chanan. Všickni ti synové Azelovi.
39 Ana a Eseki mʼbale wake anali awa: Mwana wake woyamba Ulamu, wachiwiri Yeusi ndipo wachitatu Elifeleti.
Synové pak Ezeka, bratra jeho: Ulam prvorozený jeho, Jehus druhý, a Elifelet třetí.
40 Ana a Ulamu anali asilikali olimba mtima amene amadziwa kugwiritsa ntchito uta. Iwo anali ndi ana ndi adzukulu ambiri ndipo onse analipo 150. Onsewa anali adzukulu a Benjamini.
A byli synové Ulamovi muži udatní a střelci umělí, kteříž měli mnoho synů a vnuků až do sta a padesáti. Všickni ti byli z synů Beniaminových.

< 1 Mbiri 8 >