< 1 Mbiri 1 >

1 Adamu, Seti, Enosi
[從亞當到亞巴郎的族譜]亞當、舍特、厄諾士、
2 Kenani, Mahalaleli, Yaredi,
刻南、瑪拉肋耳、耶勒得、
3 Enoki, Metusela, Lameki, Nowa.
哈諾客、默突舍拉、
4 Ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti.
諾厄、閃、含和耶斐特。
5 Ana aamuna a Yafeti anali: Gomeri, Magogi, Madai, Yavani, Tubala, Mesaki ndi Tirasi.
耶斐特的子孫:哥默爾、瑪哥格、瑪待、雅汪、突巴耳、默舍客和提辣斯。
6 Ana aamuna a Gomeri anali: Asikenazi, Rifati ndi Togarima
哥默爾的子孫:阿市革納次、黎法特和托加爾瑪。
7 Ana aamuna a Yavani anali: Elisa, Tarisisi, Kitimu ndi Rodanimu.
雅汪的子孫:厄里沙、塔爾史士、基廷和多丹。
8 Ana aamuna a Hamu anali: Kusi, Miziraimu, Puti ndi Kanaani
含的子孫:雇士、米茲辣殷、普特和客納罕。
9 Ana aamuna a Kusi anali: Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka Ana aamuna a Raama anali: Seba ndi Dedani.
雇士的子孫;色巴、哈威拉、撒貝達、辣阿瑪和撒貝特加。辣阿瑪的子孫:舍巴和德丹。
10 Kusi anali abambo a Nimurodi amene anali wankhondo wamphamvu kwambiri pa dziko lapansi.
雇士生尼默洛得;他是世界上第一個強人。
11 Igupto ndiye kholo la Aludi, Aanami, Alehabu, Anafutu,
米茲辣殷生路丁人、阿納明人、肋哈賓人、納斐突歆人、
12 Apaturusi, Akasilu (kumene kunachokera Afilisti) ndi Akafitori.
帕特洛斯人、加斯路人和加非托爾人,即培肋舍特的祖先。
13 Kanaani anabereka mwana wake wachisamba Sidoni, ndipo anaberekanso Ahiti,
克納罕生長子漆冬,次為赫特、
14 Ayebusi, Aamori, Agirigasi
耶步斯人、阿摩黎人、基爾加史人、
15 Ahivi, Aariki, Asini
希威人、阿爾克人、息尼人、
16 Aaravadi, Azemari ndi Ahamati.
阿爾瓦得人、責瑪黎人和哈瑪特人。
17 Ana aamuna a Semu anali: Elamu, Asuri, Aripakisadi, Ludi ndi Aramu. Ana aamuna a Aramu anali: Uzi, Huri, Geteri ndi Mesaki.
閃的子孫:厄藍、亞述、阿帕革沙得、路得、阿蘭。阿蘭的子孫:伍茲胡耳、革特爾和默舍客。
18 Aripakisadi anabereka Sela ndipo Selayo anabereka Eberi:
阿帕革沙得生舍特,舍特生厄貝爾。
19 Eberi anabereka ana aamuna awiri: wina anamutcha Pelegi, chifukwa pa nthawiyo anthu a pa dziko lapansi anagawikana. Dzina la mʼbale wake linali Yokitani.
厄貝爾生了兩個兒子:長子名叫培肋格,因為在他的時代,世界分裂了;他的兄弟明叫約刻堂。
20 Yokitani anabereka Alimodadi, Selefi, Hazari-Maveti, Yera,
約刻堂生阿耳摩達得、舍肋夫、哈匝瑪委特、耶辣、
21 Hadoramu, Uzali, Dikila
哈多蘭、烏匝耳、狄刻拉、
22 Obali, Abimaeli, Seba,
厄巴耳、阿彼瑪耳、舍巴、
23 Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onsewa anali ana aamuna a Yokitani.
敖非爾、哈威拉和約巴布:這些人都是約刻堂的子孫。
24 Semu, Aripakisadi, Sela
閃阿帕革沙得、舍拉、
25 Eberi, Pelegi, Reu
厄貝爾、培肋格、勒伍、
26 Serugi, Nahori, Tera
色魯格、納曷爾、特辣黑、
27 ndi Abramu (amene ndi Abrahamu).
亞巴郎即亞貝辣罕。[亞巴郎的後代]
28 Ana a Abrahamu ndi awa: Isake ndi Ismaeli.
亞巴郎的兒子是依撒格和依市瑪耳。
29 Zidzukulu zake zinali izi: Nebayoti ndiye anali mwana woyamba wa Ismaeli, kenaka Kedara, Adibeeli, Mibisamu,
以下是他們的後裔:依市瑪耳的長子是乃巴約特,次為刻達爾、阿德貝米、米貝散、
30 Misima, Duma, Masa, Hadadi, Tema,
米市瑪、杜瑪、瑪薩、哈達得、特瑪、
31 Yeturi, Nafisi ndi Kedema. Awa anali ana a Ismaeli.
耶突爾、納菲士和刻德瑪:以上是依市瑪耳的兒子。
32 Ana a Ketura mzikazi wa Abrahamu anali awa: Zimurani, Yokisani, Medani, Midiyani, Isibaki ndi Suwa. Ana a Yokisani ndi awa: Seba ndi Dedani
亞巴郎的妾刻突辣所生的兒子:齊默郎、約刻商、默丹、米德楊、依市巴克和叔哈;約刻商的兒子:舍巴和德丹。
33 Ana aamuna a Midiyani anali, Efai, Eferi, Hanoki, Abida ndi Elida. Onsewa anali zidzukulu za Ketura.
米德楊的兒子:厄法、厄斐爾、哈諾客、阿彼達和厄耳達阿:以上都是刻突辣的子孫。
34 Abrahamu anabereka Isake. Ana a Isake anali awa: Esau ndi Israeli.
亞巴郎生依撒格;依撒格生厄撒烏和以色列。
35 Ana aamuna a Esau anali awa: Elifazi, Reueli, Yeusi, Yolamu ndi Kora.
厄撒烏的兒子:厄里法次、勒烏耳、耶烏士、雅藍和科辣黑。
36 Ana a Elifazi anali awa: Temani, Omari, Zefo, Gatamu ndi Kenazi: Amene anabereka ndi Timna: Amaleki.
厄里法次的子孫:特曼、敖瑪爾、則非、加堂、刻納次、提默納和阿瑪肋克。
37 Ana a Reueli anali awa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza.
勒烏耳的子孫:納哈特、則辣黑、沙瑪和米匝。[色依爾的後裔]
38 Ana a Seiri anali awa: Lotani, Sobala, Zibeoni, Ana, Disoni, Ezeri ndi Disani.
色依爾的子孫:羅堂、芍巴耳、漆貝紅、阿納、狄雄、厄責爾和狄商。
39 Ana aamuna a Lotani anali awa: Hori ndi Homamu. Timna anali mlongo wake wa Lotani.
羅堂的兒子:曷黎和曷曼;羅堂的姊妹:提默納。
40 Ana aamuna a Sobala anali awa: Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu. Ana aamuna a Zibeoni anali awa: Ayiwa ndi Ana.
芍巴耳的兒子:阿里楊、瑪納哈特、厄巴耳、舍非和敖南。漆貝紅的兒子:阿雅和阿納。
41 Mwana wa Ana anali Disoni. Ana a Disoni anali awa: Hemudani, Esibani, Itirani ndi Kerani
阿納的兒子:狄雄;狄雄的兒子:哈默郎、厄市班、依特郎和革郎。
42 Ana aamuna a Ezeri anali awa: Bilihani, Zaavani ndi Yaakani. Ana aamuna a Disani anali awa: Uzi ndi Arani.
厄責爾的兒子:彼耳漢、匝汪和阿甘。狄商的兒子:伍茲和阿郎。[厄東的君王]
43 Awa ndi mafumu amene ankalamulira dziko la Edomu, mfumu iliyonse ya Israeli isanayambe kulamulira kumeneko: Bela mwana wa Beori, mzinda wake ankawutcha Dinihaba.
以下是在以色列子民未有君王統治以前,統治厄東地的君王:貝敖爾的兒子貝拉;他的京城名叫丁哈巴。
44 Bela atamwalira, Yobabu mwana wa Zera wochokera ku Bozira analowa ufumu mʼmalo mwake.
貝拉死後,波責辣人則辣黑的兒子約巴布繼他為王。
45 Yobabu atamwalira, Husamu wochokera ku dziko la Atemani, analowa ufumu mʼmalo mwake.
約巴布死後,特曼地人胡商繼他為王。
46 Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani mʼdziko la Mowabu, analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Aviti.
胡商死後,貝達得的兒子哈達得繼他為王。他曾在摩阿布平原擊敗了米德楊人;他的京城名叫阿威特。
47 Hadadi atamwalira, Samila wochokera ku Masireka analowa ufumu mʼmalo mwake.
哈達得死後,瑪斯勒卡人撒默拉繼他為王。
48 Samila atamwalira, Sauli wochokera ku Rehoboti wa ku Mtsinje analowa ufumu mʼmalo mwake.
撒默拉死後,河間的勒曷波特人沙烏耳繼他為王。
49 Sauli atamwalira, Baala-Hanani mwana wa Akibori analowa ufumu mʼmalo mwake.
沙烏耳死後,阿革波爾的兒子巴耳哈南繼他為王。
50 Pamene Baala-Hanani anamwalira, Hadadi analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Pau, ndipo dzina la mkazi wake linali Mehatabeli mwana wa Matiredi, mwana wamkazi wa Me-Zahabu.
巴耳哈南死後,哈達得繼他為王,他的京城名叫帕依,他的妻子名叫默塔貝耳,是默匝哈布人瑪特勒得的女兒。[厄東的族長]
51 Hadadi anamwaliranso. Mafumu a ku Edomu anali: Timna, Aliva, Yeteti,
哈達得死後,為厄東族長的是:提默納族長,阿里雅族長,耶太特族長,
52 Oholibama, Ela, Pinoni,
敖曷里巴族長,厄拉族長,丕農足長,
53 Kenazi, Temani, Mibezari,
刻納次族長,特曼族長,米貝匝爾族長,
54 Magidieli ndi Iramu. Awa anali mafumu a ku Edomu.
瑪革狄耳族長和依蘭族長:以上是厄東的族長。

< 1 Mbiri 1 >